Комментарии:
I wish I was there
ОтветитьMadala iweyo siukuziwa zimene ukune na
ОтветитьAkatolika mavuto amene akuwakhudza kwambili 😂😂😂😂😂😂😂😂
ОтветитьKubweletsa anthu akuba boma kuphana ndi kuba dziko kuno Akatolika mukudziwapo kathu 😂😂😂😂😂
ОтветитьShame on Muslims
ОтветитьMapunziro amenewo ofunika thawing yokwanira,tidzayamba kuphunzitsa after chisankho for 2030 not now....this time ndi manual manual
ОтветитьAm here chifukwa Cha Traore basi❤
ОтветитьChe Mandota uja samapangadala kkkkkkkkkk
ОтветитьDeya wafika pa umufuti eti?
ОтветитьPeter Banda
ОтветитьYa Traore mwaisiya
ОтветитьIbrahim kumalawi tili nayo ndi Denis mahata
ОтветитьMutiphuzise kaye zachimashini
ОтветитьKkkkk koma amalawi ndiosekesa ukawone mumene wavalila shehe ngati ndiku maluya kaliwonela kuiwala chikhalidwe chake
ОтветитьIne ndimavesela ndi chidwi ndimaona ngati pali nkhani ya Ibrahim
ОтветитьAkatolika nawo kuvala ngati ndi aku Italy za ziiii
ОтветитьTraure........traure
Ответить